Mavuto A Padziko Lonse. Germany. Nthawi Yochita | Msonkhano Wapaintaneti, Marichi 18, 2023

1 year ago
12

Tikukhala m'nthawi yamavuto apadziko lonse lapansi omwe akukokera pasi dziko la Germany ndikulipangit6sa kukusakhazikika komanso kusatsimikizika. Komabe, tikuyembekezera tsogolo labwino kwa ife ndi ana athu. Kodi zimenezi n’zoona?

Lero, mothandizidwa ndi akatswiri, tiyesetsa kuti tidziwe momwe tingathetsere mavutowa. Creative Society polojekiti ya pa intaneti t ndi mwayi weniweni wopeza njira yothetsera vutoli.

Msonkhano “Mavuto a Padziko Lonse. Germany. Nthawi yochita kanthu” ikupatsani chidziwitso pamitu iyi:

mavuto a magetsi
kukwera mitengo ya zinthu ndi mavutoo a zachuma ku Germany
mavuto a zachikhalidwe
mavuto a za nyengo mu mzaka zikubwerazi
njira zothetsera mavutowa pa nthawi yochoka mu consumerist fomart kupita mu Creative Society

Tikukuitanani kuti mudzagwirizane nafe pomanga tsogolo labwino la tonsefe!

💠 Tsamba lovomerezeka la Creative Society polojekiti ya dziko lonse: https://creativesociety.com

📩 Imelo: info@creativesociety.com

Loading comments...